Quraan Icon Welengani Qur'aan Yolemekezeka
Yomasuliridwa ndi Sheykh Khalid Ibrahim

Surah Al-Ankaboot (العنكبوت)

Sura iyi idavumbulutsidwa ku Makka. Aya zake zilipo 69. Aya 1 mpaka 11 zidavumbulutsidwa ku Madina. Surayi yayamba ndi kufotokoza kuti nkofunika kwa okhulupirira kuyesedwa mayeso ndi masautso, monga nkhondo, kuti chikhulupiriro chawo chikhale chokhwima. Ndipo yalangiza munthu kuti achitire zabwino makolo ake ndi kuchita jihadi (nkhondo) panjira ya Chauta ...

Welengani surah yonse...

recommended news item

Islam Fast Facts
-- published by CNN World on Aug. 25, 2017, 6:02 p.m.